Salimo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akumbukire nsembe zanu zonse zimene munapereka monga mphatso.Alandire mosangalala* nsembe zanu zopsereza. (Selah)
3 Akumbukire nsembe zanu zonse zimene munapereka monga mphatso.Alandire mosangalala* nsembe zanu zopsereza. (Selah)