Salimo 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumuyo inakupemphani moyo wautali ndipo munaipatsadi.+Munaipatsa moyo wautali* kuti ikhale mpaka kalekale.
4 Mfumuyo inakupemphani moyo wautali ndipo munaipatsadi.+Munaipatsa moyo wautali* kuti ikhale mpaka kalekale.