Salimo 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu onse amene amandiona amandiseka.+Iwo amandinyogodola nʼkumapukusa mitu yawo mondinyoza nʼkumati:+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:7 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 15
7 Anthu onse amene amandiona amandiseka.+Iwo amandinyogodola nʼkumapukusa mitu yawo mondinyoza nʼkumati:+