Salimo 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu ndi amene munanditulutsa mʼmimba,+Ndinu amene munandichititsa kumva kuti ndine wotetezeka pamene ndinkayamwa mabere a mayi anga.
9 Inu ndi amene munanditulutsa mʼmimba,+Ndinu amene munandichititsa kumva kuti ndine wotetezeka pamene ndinkayamwa mabere a mayi anga.