Salimo 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndingathe kuwerenga mafupa anga onse.+ Adaniwo akuona zimenezi ndipo akundiyangʼanitsitsa.