Salimo 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma inu Yehova, musakhale kutali ndi ine.+ Inu ndinu mphamvu zanga, ndithandizeni mofulumira.+