Salimo 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Inu amene mumaopa Yehova, mutamandeni! Inu nonse mbadwa* za Yakobo, mʼpatseni ulemerero!+ Muopeni, inu nonse mbadwa* za Isiraeli.
23 Inu amene mumaopa Yehova, mutamandeni! Inu nonse mbadwa* za Yakobo, mʼpatseni ulemerero!+ Muopeni, inu nonse mbadwa* za Isiraeli.