Salimo 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anthu onse olemera* padziko lapansi adzadya ndipo adzamuweramira.Anthu onse amene amabwerera kufumbi adzagwada pamaso pake,Ndipo palibe aliyense wa iwo amene angapulumutse moyo wawo.
29 Anthu onse olemera* padziko lapansi adzadya ndipo adzamuweramira.Anthu onse amene amabwerera kufumbi adzagwada pamaso pake,Ndipo palibe aliyense wa iwo amene angapulumutse moyo wawo.