Salimo 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mumandipatsa chakudya patebulo pamaso pa adani anga.+ Ndimatsitsimulidwa mukandidzoza mafuta kumutu.+Kapu yanga ndi yodzaza bwino.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:5 Nsanja ya Olonda,11/1/2005, ptsa. 19-207/1/1988, ptsa. 26-27
5 Mumandipatsa chakudya patebulo pamaso pa adani anga.+ Ndimatsitsimulidwa mukandidzoza mafuta kumutu.+Kapu yanga ndi yodzaza bwino.+