Salimo 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aliyense amene ndi wosalakwa komanso wopanda chinyengo mumtima mwake,+Amene sanalumbire mwachinyengo potchula moyo Wanga,*Kapena kulumbira pofuna kupusitsa anthu ena.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:4 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2017, tsa. 4
4 Aliyense amene ndi wosalakwa komanso wopanda chinyengo mumtima mwake,+Amene sanalumbire mwachinyengo potchula moyo Wanga,*Kapena kulumbira pofuna kupusitsa anthu ena.+