Salimo 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye adzalandira madalitso kuchokera kwa Yehova,+Komanso chilungamo kuchokera kwa Mulungu amene amamupulumutsa.+
5 Iye adzalandira madalitso kuchokera kwa Yehova,+Komanso chilungamo kuchokera kwa Mulungu amene amamupulumutsa.+