-
Salimo 24:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Umenewu ndi mʼbadwo wa anthu amene amafunafuna Mulungu,
Mʼbadwo wa anthu amene amafunafuna nkhope yanu, inu Mulungu wa Yakobo. (Selah)
-