Salimo 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tukulani mitu yanu, inu mageti,+Tsegukani,* inu makomo akale,Kuti Mfumu yaulemerero ilowe!+