Salimo 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi Mfumu yaulemerero imeneyi ndi ndani? Ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Iye ndi Mfumu yaulemerero.+ (Selah)
10 Kodi Mfumu yaulemerero imeneyi ndi ndani? Ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Iye ndi Mfumu yaulemerero.+ (Selah)