Salimo 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha dzina lanu, inu Yehova,+Mundikhululukire tchimo langa, ngakhale kuti ndi lalikulu.