Salimo 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiweruzeni, inu Yehova, chifukwa ndimachita zinthu mokhulupirika.+Nthawi zonse ndimadalira inu Yehova.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:1 Nsanja ya Olonda,12/1/2004, ptsa. 13-148/15/2000, tsa. 27
26 Ndiweruzeni, inu Yehova, chifukwa ndimachita zinthu mokhulupirika.+Nthawi zonse ndimadalira inu Yehova.+