Salimo 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova, ndimvetsereni pamene ndikuitana.+Ndikomereni mtima ndipo mundiyankhe.+