Salimo 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mʼpatseni Yehova zimene akuyenera kulandira, inu ana a amphamvu,Mʼpatseni Yehova zimene akuyenera kulandira chifukwa cha ulemerero ndi mphamvu zake.+
29 Mʼpatseni Yehova zimene akuyenera kulandira, inu ana a amphamvu,Mʼpatseni Yehova zimene akuyenera kulandira chifukwa cha ulemerero ndi mphamvu zake.+