Salimo 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye akuchititsa Lebanoni* kuti adumphedumphe ngati mwana wa ngʼombe,Komanso Sirioni+ kuti adumphedumphe ngati mwana wa ngʼombe yakutchire. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:6 Nsanja ya Olonda,8/15/1986, tsa. 9
6 Iye akuchititsa Lebanoni* kuti adumphedumphe ngati mwana wa ngʼombe,Komanso Sirioni+ kuti adumphedumphe ngati mwana wa ngʼombe yakutchire.