Salimo 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova wakhala pampando wake wachifumu pamwamba pa madzi osefukira,*+Yehova ndi Mfumu ndipo adzalamulira mpaka kalekale.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:10 Nsanja ya Olonda,5/15/2006, tsa. 20
10 Yehova wakhala pampando wake wachifumu pamwamba pa madzi osefukira,*+Yehova ndi Mfumu ndipo adzalamulira mpaka kalekale.+