Salimo 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova adzapatsa anthu ake mphamvu.+ Yehova adzadalitsa anthu ake powapatsa mtendere.+