Salimo 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova, pa nthawi imene munkasangalala nane,* munachititsa kuti ndikhale wamphamvu ngati phiri.+ Koma mutabisa nkhope yanu, ndinachita mantha.+
7 Inu Yehova, pa nthawi imene munkasangalala nane,* munachititsa kuti ndikhale wamphamvu ngati phiri.+ Koma mutabisa nkhope yanu, ndinachita mantha.+