Salimo 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi imfa yanga ili* ndi phindu lanji? Kodi pali phindu lanji ngati nditatsikira kudzenje la manda?+ Kodi fumbi lingakutamandeni?+ Kodi lingalengeze kuti inu ndinu wokhulupirika?+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:9 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),2/2023, tsa. 21
9 Kodi imfa yanga ili* ndi phindu lanji? Kodi pali phindu lanji ngati nditatsikira kudzenje la manda?+ Kodi fumbi lingakutamandeni?+ Kodi lingalengeze kuti inu ndinu wokhulupirika?+