Salimo 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikomereni mtima inu Yehova, chifukwa ndavutika kwambiri. Maso anga afooka chifukwa cha chisoni,+ chimodzimodzinso thupi langa lonse.*+
9 Ndikomereni mtima inu Yehova, chifukwa ndavutika kwambiri. Maso anga afooka chifukwa cha chisoni,+ chimodzimodzinso thupi langa lonse.*+