Salimo 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndamva mphekesera zambiri zoipa.Ndikuchita mantha chifukwa ndikuopsezedwa kuchokera kumbali zonse.+ Akasonkhana pamodzi kuti alimbane nane,Amakonza chiwembu kuti achotse moyo wanga.+
13 Ndamva mphekesera zambiri zoipa.Ndikuchita mantha chifukwa ndikuopsezedwa kuchokera kumbali zonse.+ Akasonkhana pamodzi kuti alimbane nane,Amakonza chiwembu kuti achotse moyo wanga.+