Salimo 31:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndikomereni mtima, ine mtumiki wanu.+ Ndipulumutseni ndi chikondi chanu chokhulupirika.