Salimo 31:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mudzawabisa mʼmalo otetezeka pafupi ndi inu,+Kuwachotsa kwa anthu amene awakonzera chiwembu.Mudzawabisa mʼmalo anu otetezekaKuti anthu amene akuwanyoza asawapeze.*+
20 Mudzawabisa mʼmalo otetezeka pafupi ndi inu,+Kuwachotsa kwa anthu amene awakonzera chiwembu.Mudzawabisa mʼmalo anu otetezekaKuti anthu amene akuwanyoza asawapeze.*+