Salimo 33:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Fuulani mosangalala chifukwa cha Yehova,+ olungama inu. Mʼpoyenera kuti olungama atamande Mulungu.
33 Fuulani mosangalala chifukwa cha Yehova,+ olungama inu. Mʼpoyenera kuti olungama atamande Mulungu.