Salimo 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muimbireni nyimbo yatsopano.+Imbani mwaluso choimbira cha zingwe ndipo muzifuula mosangalala.