Salimo 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa mawu a Yehova ndi oona,+Ndipo chilichonse chimene amachita ndi chodalirika.