Salimo 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dziko lonse lapansi liope Yehova.+ Anthu onse okhala panthaka ya dziko lapansi achite naye mantha.