Salimo 33:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye ndi amene amaumba mitima ya anthu onse,Ndipo amafufuza ntchito zawo zonse.+