Salimo 33:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mulungu amachititsa kuti mitima yathu isangalale,Chifukwa timadalira dzina lake loyera.+