-
Salimo 35:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ndinkayendayenda ndikulira ngati kuti ndikulira maliro a mnzanga kapena mchimwene wanga,
Ndinkawerama chifukwa cha chisoni ngati munthu amene akulira maliro a mayi ake.
-