-
Salimo 35:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Koma nditapunthwa anasangalala ndipo anasonkhana pamodzi.
Anasonkhana pamodzi kuti andibisalire nʼkundiukira.
Anandikhadzulakhadzula ndipo sanakhale chete.
-