Salimo 35:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mukatero, ndidzakuyamikirani mumpingo waukulu.+Ndidzakutamandani pakati pa anthu ambiri.