Salimo 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Musalole kuti anthu amene amadana nane popanda chifukwa+ asangalale chifukwa cha mavuto anga.Musalole kuti anthu amene amadana nane popanda chifukwa andipsinyire diso mondinyoza.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 35:19 Nsanja ya Olonda,5/15/2006, tsa. 208/15/1986, tsa. 9
19 Musalole kuti anthu amene amadana nane popanda chifukwa+ asangalale chifukwa cha mavuto anga.Musalole kuti anthu amene amadana nane popanda chifukwa andipsinyire diso mondinyoza.+