Salimo 35:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chifukwa iwo salankhula mwamtendere,Koma mwachinyengo, amakonzera chiwembu anthu okonda mtendere amʼdzikoli.+
20 Chifukwa iwo salankhula mwamtendere,Koma mwachinyengo, amakonzera chiwembu anthu okonda mtendere amʼdzikoli.+