Salimo 35:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu Yehova, mwaona zimenezi. Choncho musakhale chete.+ Inu Yehova, musakhale kutali ndi ine.+