Salimo 35:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Inu Yehova Mulungu wanga, mundiweruze mogwirizana ndi mfundo zanu zolungama,+Musalole kuti adani anga asangalale chifukwa cha mavuto anga.
24 Inu Yehova Mulungu wanga, mundiweruze mogwirizana ndi mfundo zanu zolungama,+Musalole kuti adani anga asangalale chifukwa cha mavuto anga.