Salimo 35:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndipo lilime langa lidzafotokoza* za chilungamo chanu,+Komanso kukutamandani tsiku lonse.+