Salimo 36:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Uchimo umalankhula mumtima mwa munthu woipa, nʼkumuuza zochita.Maso ake saona chifukwa choopera Mulungu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:1 Nsanja ya Olonda,3/15/1989, ptsa. 16-17
36 Uchimo umalankhula mumtima mwa munthu woipa, nʼkumuuza zochita.Maso ake saona chifukwa choopera Mulungu.+