-
Salimo 36:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ngakhale ali pabedi lake, amakonza chiwembu kuti apweteke anzake.
Amayenda panjira yoipa,
Ndipo sapewa kuchita zinthu zoipa.
-