Salimo 36:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova, chikondi chanu chokhulupirika chafika kumwamba.+Kukhulupirika kwanu kwafika mpaka mʼmitambo.
5 Inu Yehova, chikondi chanu chokhulupirika chafika kumwamba.+Kukhulupirika kwanu kwafika mpaka mʼmitambo.