Salimo 36:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Mulungu, chikondi chanu chokhulupirika ndi chamtengo wapatali!+ Ana a anthu amabisala mumthunzi wa mapiko anu.+
7 Inu Mulungu, chikondi chanu chokhulupirika ndi chamtengo wapatali!+ Ana a anthu amabisala mumthunzi wa mapiko anu.+