Salimo 37:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Yehova adzamuseka,Chifukwa akudziwa kuti mapeto ake adzafika.+