-
Salimo 37:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Pa nthawi ya tsoka sadzachita manyazi,
Ndipo pa nthawi ya njala adzakhala ndi chakudya chochuluka.