Salimo 37:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Nthawi zonse amakongoza ena zinthu zake mokoma mtima,+Ndipo ana ake adzalandira madalitso.