Salimo 38:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Thupi langa lonse likudwala* chifukwa cha mkwiyo wanu. Mʼmafupa anga mulibe mtendere chifukwa cha tchimo langa.+
3 Thupi langa lonse likudwala* chifukwa cha mkwiyo wanu. Mʼmafupa anga mulibe mtendere chifukwa cha tchimo langa.+