Salimo 38:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa ine ndinayembekezera inu Yehova.+Ndipo inu Yehova Mulungu wanga, munandiyankha.+